Tisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewa

By Thru the Bible Chichewa

Listen to a podcast, please open Podcast Republic app. Available on Google Play Store and Apple App Store.


Category: Christianity

Open in Apple Podcasts


Open RSS feed


Open Website


Rate for this podcast

Subscribers: 0
Reviews: 0
Episodes: 261

Description

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera pologalamu imodzi patsiku kuyambira lolemba mpaka lachisanu. Ngati mungakwanitse kutsatira ndondomekoyi, pakutha kwa zaka zisanu mudzakhala kuti mwawerenga Baibulo lonse.

Episode Date
Yoasi Akhala Mfumu Ndi Ulamuliro Wake
Oct 22, 2024
Yehu Akhala Mfumu Ya Israyeli Ndi Chilango Pa Nyumba Ya Ahabu
Oct 21, 2024
Elisa Akwaniritsa Malonjezo Ake Ndi Chilango Kwa Oipa
Oct 18, 2024
Elisa Ayandamitsa Nkhwangwa Pa Madzi Ndi Chiwembu Cha Elisa Ku
Oct 17, 2024
Mbiri Ya Namaani Wa Ku Syria
Oct 16, 2024
Elisa Alowa M’malo Mwa Eliya Ndi
Oct 15, 2024
Moto Wa Kumwamba Woteteza Eliya Kwa Ahaziya Ndipo Eliya Akwera Kumwamba
Oct 14, 2024
Ahabu Ndi Munda Wa Naboti; Ahabu Ndi Mneneri Mikaya
Oct 11, 2024
Eliya Ali Pansi Pa Mtengo Wa Tsanya: Israyeli Amenyana Ndi Syria
Oct 10, 2024
Eliya Adzudzula Ahabu Ndipo Yehova Atsutsana Ndi Baala Pa Phiri La Kalimeri
Oct 09, 2024
Ukwati Wa Yezeberi Ndi Ahabu Ndi Kuti Eliya Alengeza Za Chilala Kwa Zaka Zitatu
Oct 08, 2024
Imfa Ya Rehabiamu Ndi Yerobiamu; Mafumu A Ufumu Wogawika
Oct 07, 2024
Chilango Pa Yerobiamu Ndi Yuda
Oct 04, 2024
Zinthu Zochititsa Manyazi Ndi Imfa Ya Solomoni; Kugawika Kwa Ufumu Pakati Pa Rehabiamu Ndi Yerobiamu
Oct 03, 2024
Ntchito Yomanga Kachisi Ndi Mwambo Wopereka Kachisi
Oct 02, 2024
Ntchito Yomanga Kachisi Ndi
Oct 01, 2024
Kukonzekera Ndi Kumanga Kachisi Wa Mulungu
Sep 30, 2024
Chopempha Cha Solomoni; Pemphero Lake Liyankhidwa Ndi Ukulu Wa Ufumu Wake
Sep 27, 2024
Upangiri Wa Davide Kwa Solomoni Ndipo Solomoni Apempha Nzeru
Sep 26, 2024
Kulephera Kwa Chiwembu Cha Adoniya; Solomoni Adzozedwa Mfumu; Malangizo A Davide Kwa Solomoni.
Sep 25, 2024
Mau Otsiriza A Davide; Anyamata A Davide Amphamvu Ndi Chiwerengero
Sep 24, 2024
Njala Mu Israyeli, Agibeoni Abwezera Nkhondo Ndi Afilisti
Sep 23, 2024
Davide Abwezeretsedwa Pa Ufumu Wake Ndipo Seeba Aukira
Sep 20, 2024
Nkhondo Pakati Pa Davide Ndi Absalomu
Sep 19, 2024
Abisalomu Aukira Atate Wake, Davide
Sep 18, 2024
Uchimo Wa Ana A Davide; Amoni Ndi Absalomo
Sep 17, 2024
Natani Adzudzula Davide Chifukwa Cha Uchimo Wake Ndipo Davide Alapa Chimolo
Sep 16, 2024
Davide Ayambana Ndi Ammoni Ndi Asuri Ndi Uchimo Uwiri Waukulu Wa Davide
Sep 13, 2024
Ufumu Wa Davide Ukhala Wamphamvu Ndipo Davide Akhala Pa Ubwezi Ndi Mefiboseti
Sep 12, 2024
Pangano La Mulungu Pa Kumanga Nyumba Ya Davide
Sep 11, 2024
Njira Zoyenera Ndi Zolakwika Zomwe Davide Anatenga Pobweretsa Likasa Ku Yerusalemu
Sep 10, 2024
Davide Akhazikitsidwa Mfumu Wa Israyeli Yense
Sep 09, 2024
Davide Akhazikitsidwa Mfumu
Sep 06, 2024
Sauli Ndi Jonatani Aphedwa Ku Nkhondo
Sep 05, 2024
Moyo Wa Davide Pamene Ali Pakati Pa Afilisti
Sep 04, 2024
Davide Abwerera Kudziko La Afilisti Pamene Sauli Apita Kwa Sing’anga
Sep 03, 2024
Davide Akwatira Abigayeli Ndipo Davide Asiya Kupha Sauli Kachiwiri
Sep 02, 2024
Chitetezo Ndi Chisamaliro Cha
Aug 30, 2024
Davide Asonkhanitsa Anyamata
Aug 29, 2024
Mulungu Alanga Davide; Ndipo Davide Apempha Ansembe Kuti Amuthandize
Aug 28, 2024
Mulungu Akuphunzitsa Davide; Sauli Afuna Kupha Davide; Ndipo Jonatani Amuthandiza Kuthawa
Aug 27, 2024
Davide Adzonzedwa Ndipo Akupha Goliati
Aug 26, 2024
Kusamvera Kwa Sauli Pa Agagi Ndipo Samueli Mudzudzula
Aug 23, 2024
Sauli Apandukira Mulungu; Yonatani Apambana Pankhondo Ya Afilisti; Komanso Kuipa Kwa Lamulo Lofulumira La Sauli
Aug 22, 2024
Sauli Agonjetsa Amoni Ndi Kuchoka Kwa Udindo Kwa Samueli Kupita Kwa Sauli
Aug 21, 2024
Sauli Asankhidwa Ndi Kudzozedwa
Aug 20, 2024
Chilango Cha Mulungu Pa Afilisti;
Aug 19, 2024
Kuitanidwa Kwa Samueli; Chilango Cha Mulungu Pa Eli Ndi Ana Ake Chikwanitsidwa; Komanso Chilango Cha Mulungu Pa Afilisti
Aug 16, 2024
Pemphero La Hana La Ulosi; Ana A Eli Woipa; Mwana Samueli M’kachis
Aug 15, 2024
Chiyambi Cha Bukhuli, Kubadwa Kwa Samueli
Aug 14, 2024
Chifundo Cha Anthu Akunja Machilitso Ya Yesu; Ulendo Wotsiriza Ku Roma Ndi Ayuda
Aug 13, 2024
Ulendo Wa Paulo Wamasautso Ukuptilira Panyanja Paoneka Mwera Ndi Kuonongeka Kwa Ngalawa
Aug 12, 2024
Paulo Atsika Ku Kaisareya Ndi Kuyamba Ulendo Wake Wa Pa Nyanja Wopita Ku Roma
Aug 09, 2024
Masautso A Paulo Akupitilira Pa Ulendo Wake Wa Ku Roma, Kuchitira Umboni Uitanidwa Ku Kaisareya
Aug 08, 2024
Ulendo Woopsa Wa Paulo Ukupitilira Ndi Umboni Ku Kaisareya
Aug 07, 2024
Ulendo Woopsa Wa Paulo Ku Roma Ukupitilira
Aug 06, 2024
Ulendo Woopsa Wa Paulo Ku Roma Ukupitirira
Aug 05, 2024
Zobvuta Zokonzedwa Ndi A Yuda Zikupitilira Pa Ulendo Wa Paulo Ku Aroma
Aug 02, 2024
Ulendo Wamasautso Wa Paulo Ku Roma
Aug 01, 2024
Maulendo A Paulo, Zochenjeza Kwa Paulo Ndi Kuti Akhala Ndi A Yuda
Jul 31, 2024
Utumiki Wa Paulo Ndi Umboni Wake Kwa Akulu Ku Efeso
Jul 30, 2024
Utumiki Wa Paulo Uchita Bwino Pa Zaka Ziwiri Mu Efeso; Gulu La Oukira Ndimlembi Abwino; Paulo Apita Ku Greece Ndi Ku Korinto
Jul 29, 2024
Paulo Ku Korinto Ndi Bvuto La Ayuda; Nthawi Pang’ono Ku Aefeso; Ulendo Wachitatu Wa Paulo
Jul 26, 2024
Paulo Alalikira Ku Atene Mkati
Jul 25, 2024
Uthenga Wabwino Ulandiridwa Ku Atesalonika Ndi Ku Berea; Ayuda
Jul 24, 2024
Paulo; Kuitanidwa Ku Ulaya Ndi Zochitika Ku Afilipi
Jul 23, 2024
Gawo La Chiwiri Loona Ngati M’dulidwe Ndi Lamulo La Mose Ndizofunika Kapena Ayi; Komanso Paulo Ndi Barnaba Apatukana
Jul 22, 2024
Gawo Loyamba La Loona Ngati Mdulidwe Ndi Lamulo La Mose Ndilofunika Kapena Ayi
Jul 19, 2024
Uthenga Wabwino Ulalikidwa Ku Ikoniyo, Lustra, Ndi Derbe; Kubwereranso Ku Lustra Ndi Ikoniyo Ndi Antiokeya; Ndi Kubwerera Kunyumba
Jul 18, 2024
Mulungu Aitana Barnaba Ndi Paulo; Zochitika Ku Kupro; Marko Abwerera Ndi Zochitika Ku Antiokeya
Jul 17, 2024
Petulo Atuluka Mndende, Paulo Ndi Banaba Abwelera Ku Antiyokeya
Jul 16, 2024
Mau A Petro Odziteteza Pophatikana Ndi Anthu A Amitundu Komanso Tiona Za Mpingo Wa Ku Antiokeya
Jul 15, 2024
Chipulumutso Cha A Amitundu Chikudza Ndi Mphamvu Ya Mulungu
Jul 12, 2024
Kutembenuka Mtima Kwa Saulo; Utumiki Wa Petro Ku Yopa Ndi Luda
Jul 11, 2024
Filipo Athandiza Mdindo Wa Ku Aitiopiya Kutembenuka Mtima
Jul 10, 2024
Masautso Akulu; Utumiki Wa Filipo; Chikhulupiriro Cha Simoni; Utumiki Wa Petro Ndi Yohane; Mlaliki Filipo
Jul 09, 2024
Kudzikanila Kwa Stefano Pamaso Pa Bwalo La Sanhedrin Ndi Imfa Yake
Jul 08, 2024
Udani Wa M’chikhalidwe; Kuyendetsa Mpingo Moopa Mulungu; Kukula Kwa Mpingo Muyerusalemu; Ndi Kuona Adani A Stefano
Jul 05, 2024
Kuchotsa Chodetsa Mumpingo; Kufalitsa Uthenga Kopambana Ndi Kuzunzika Kwa Mpingo Ndi Upangiri Wa Gamalieli
Jul 04, 2024
Kusakondwa Kwa Atsogoleri A Chiyuda Ndi Petro Ndi Yohane; Kuweruza Kwachilendo; Kuopseza;
Jul 03, 2024
Mphamvu za Mzimu Woyera, Petulo alalikiranso
Jul 02, 2024
Petulo ayankha otsutsana naye, Uneneri wa Yoeli; Petulo alalika Yesu anthu 3,000 nkutembenuka mtima
Jul 01, 2024
Kuyamba kwa mpingo komanso ubatizo wa Mzimu Woyera
Jun 28, 2024
Yesu alangiza Ophunzira ake, alonjeza mzimu woyera komanso za kukwera kwake
Jun 27, 2024
Mlatho komanso Mbiri ya bukhu
Jun 26, 2024
Rute mumtima komanso pakhomo la Boazi
Jun 25, 2024
Rute asankha Boazi ngati mlowamalo
Jun 24, 2024
Rute kukunkha kwa Boazi
Jun 21, 2024
Rute Apitiliza Kukunkha Chakudya M’munda Wa Boazi
Jun 20, 2024
Rute Akunkha Chakudya M’munda Wa Boazi
Jun 19, 2024
Kubwerera ku Betelehemu
Jun 18, 2024
Chiyambi, Kulowa ku Moabu
Jun 17, 2024
Dziko lilowerera pauzimu ndi pa ndale
Jun 14, 2024
Oweruza Samusoni
Jun 13, 2024
Nsanje ya Efurayimu, za oweruza ena anatu
Jun 12, 2024
Yefuta abweretsa chipambano kwa Amoni
Jun 11, 2024
Utsogoleri wakanika
Jun 10, 2024
Zaka 40 zamtendere pansi pa utsogoleri wa Gidiyoni
Jun 07, 2024
Mulungu apulumutsa Israyeli kudzera mwa Gidiyoni
Jun 06, 2024
Kulowelera kwa kachisanu ndi chimodzi
Jun 05, 2024
Nyimbo ya Debora ndi Baraki
Jun 04, 2024
Mulungu agwiritsa anthu wamba kupulumutsa Israyeli
Jun 03, 2024
Zochitika ku Israyeli atamwalira Yoshua
May 31, 2024
Uthenga womaliza wa Yoshuwa
May 30, 2024
Midzi Ya A Levi Ndi Midzi Iwiri Ya Hafu Ikhala Kum’mawa Kwa Yordano
May 29, 2024
Kumaliza Kugawa Madera Kwa Ana A Israyeli Ndi Midzi Yopulumukiramo
May 28, 2024
Kudula Malire A Malo A Mapfuko Ya Ana A Israyeli
May 27, 2024
Dziko La Kum’mawa Kwa Mtsinje Wa Yordano Ndi Gawo La Kalebe
May 24, 2024
Kutsiriza Nkhondo Ya Kum’mwera Ndi Kupita Kumpoto Kwa Kanani
May 23, 2024
A Gibeoni Ndi Nkhondo Yochokera Kum’mwera
May 22, 2024
Israyeli Alephera kugonjetsa Ai Kenaka Tiona Kupasuka kwake
May 21, 2024
Kugonjetsa Mudzi Wa Yeriko
May 20, 2024
Zinthu Zitatu Zochitika Komanso Zofunika Kwambiri
May 17, 2024
Israyeli Aoloka Mtsinje Wa Yordano
May 16, 2024
Yoswa Atenga Ulamuliro Pa Israyeli
May 15, 2024
Chiyambi Cha Bukhu La Yoswa, Yoswa Atenga Udindo Ndi
May 14, 2024
Nyimbo Ya Mose, Mdalitso Ndi Imfa Yake Ulamuliro Wake
May 13, 2024
Moyo Ndi Zabwino Kulinganiza Ndi Imfa Ndi Zoyipa; Kusintha Kwa Utsogoleri
May 10, 2024
Pangano La Dziko La Malonjezano
May 09, 2024
Malonjezo A Mulungu; Madalitso Pakumvera Ndi Tsoka Pa kusamvera
May 08, 2024
Kukwapula Wolakwa, Kuteteza Mkazi Wamasiye, Chilango Cha Amaleke, Ndi Chopereka Cha Zipatso Zoyamba
May 07, 2024
Kukhala Mu Israyeli, Ukhondo, Malamulo A Mose Pa Kuthetsa Ukwati Ndi Malamulo Wena
May 06, 2024
Chilango Chopachikidwa Pamtengo; Za
May 03, 2024
Malamulo A Nkhondo, Kupha, Amayi
May 02, 2024
Mesiya, Mneneri Woona Ndi Onama, Midzi Yopulumikira Ndi Malamulo Wena
May 01, 2024
Kumtumikira Mulungu Ndi Mtima Wonse;
Apr 30, 2024
Chaka Chopuma, Ukapolo, Madyerero Atatu, Kuweruza Ndi Kupembedza Mafano
Apr 29, 2024
Kupitiliza Za Aneneri Onama; Midzi Yonyasa; Chikhalidwe Ndi malamulo apa Chakudya ndi chakhumi
Apr 26, 2024
Lamulo Lakutenga Malo, Malo Amodzi Opembedzerapo, Malamulo A Zakudya Ndi Kuchenjeza Za Aneneri Onama
Apr 25, 2024
Kulephera Kwa Israyeli; Miyala Ya Malamulo Atsopano; Kupembedzera Kwa Mose; Kupatulidwa Kwa A Levi; Chisamaliro Cha Mulungu; Ndi Lamulo La Kutenga Malo
Apr 24, 2024
Zomwe Anachita Mulungu M’mbuyomo, Ndizimene Zimapereka Chilimbikitso Pa Zomwe Mulungu Adzachite
Apr 23, 2024
Chipulumutso Ndiubale Omwe
Apr 22, 2024
Mose Apereka Ndi Kumasuliranso Malamulo
Apr 19, 2024
Chikondi Cha Mulungu Chionekera Mwa Isarayeli Ndipo Ayenera Kuphunzitsa Ana Kupembedza Mulungu M’mzimu
Apr 18, 2024
Mose Aunikanso Za Kulephera Kwa Israyeli M’njira Zosiyana-Siyana Ndipo awalimbikitsa Kuti Amvere Mulungu
Apr 17, 2024
Chiyambi Cha Bukhu La Deuterenomo Ndi Kuona Za Uchimo WaIsrayeli Pa Kadesi Barnea
Apr 16, 2024
Mau Omaliza A Yohane Otseka Nawo Bukhu
Apr 15, 2024
Ophunzira Aona Yesu Atauka Kumanda
Apr 12, 2024
Kuuka Ku Manda Kwa Yesu Kristu
Apr 11, 2024
Imfa Ya Yesu Pa Mtanda
Apr 10, 2024
Yesu Kubwalo La Annasi Ndi Pilato
Apr 09, 2024
Yesu Agwidwa M’munda Wa Getsemane
Apr 08, 2024
Yesu Apempherera Ophunzira Wake M’nyengo Yonse
Apr 05, 2024
Yesu Apenya Mtsogolo Ndi Chiyembekezo Cha Mtanda
Apr 04, 2024
Kupitiliza Kuphunzitsa Za Mzimu Woyera
Apr 03, 2024
Yesu Achenjeza Za Kubwera Kwa Otsutsa
Apr 02, 2024
Wophunzira Ayenera Kukhala Mwa Yesu Ndi Kumumvera Iye
Apr 01, 2024
Yesu Adzitchula Kukhala Mpesa Ndipo Ophunzira Ake Ndiwo Nthambi
Mar 29, 2024
Yesu Alonjeza Mzimu Woyera
Mar 28, 2024
Yesu Alimbikitsa Ophunzira Wake
Mar 27, 2024
Yudase Achoka Ndipo Yesu Aneneratu Kuti Petro Adzamukana Iye
Mar 26, 2024
Yesu Asambitsa Mapazi Ya Ophunzira Ake
Mar 25, 2024
Yesu Alowa M’nthawi Ya Masautso
Mar 22, 2024
M’yuda Ndi Ahelene Achitira Yesu Umboni
Mar 21, 2024
Yesu Aukitsa Lazaro Kwa Akufa
Mar 20, 2024
Yesu Akonzekeretsa Ophunzira Wake Kuti Akumane Ndi Lazaro
Mar 19, 2024
Yesu Akudziula Kuti Ndiye M’busa Wabwino
Mar 18, 2024
Israyeli Akuonetsa Chithunzi Chakuti Ndikhola La Nkhosa
Mar 15, 2024
Munthu Wosaona Uja, Tsopano Waona Yesu
Mar 14, 2024
Yesu Atsegula Maso A Munthu Amene Anabadwa Ali Wakhungu
Mar 13, 2024
Yesu Akudziulura Kuti Ndiye Kuunika Kwa Dziko Lapansi
Mar 12, 2024
Yesu Akhulukira Mkazi Wogwidwa Chigololo
Mar 11, 2024
Udani Ukukula Pa Yesu
Mar 08, 2024
Yesu Apitiliza Kuphunzitsa Za Mkate Wamoyo
Mar 07, 2024
Yesu Adziulula Kuti Ndiye Mkate Wa moyo
Mar 06, 2024
Yesu Adyetsa Anthu Zikwi Zisanu (5,000) Komanso Ayenda Pa Nyanja
Mar 05, 2024
Yesu Atsimikiza Kunena Kuti Iye Ndi Atate Wake, Ali Amodzi
Mar 04, 2024
Yesu Aulura Umulungu Wake Ndipo Ayuda Atsutsana Naye
Mar 01, 2024
Chipulumutso M’mudzi Wa Samariya
Feb 29, 2024
Yesu Akumana Ndi Mkazi Pa Chitsime
Feb 28, 2024
Ulendo Wa Nikodemo Ndi Umboni Wa Yohane M’batizi
Feb 27, 2024
Yesu Agwiritsa Ntchito Mau Poyeretsa Kachisi Ndi Nkhani Ya Nikodemo
Feb 26, 2024
Ntchito Yoyamba Ya Yesu Pa Ukwati Wa Ku Kana
Feb 23, 2024
Umboni Wochitira Yesu Wa Anthu Anayi
Feb 22, 2024
Umunthu Wa Mwana Wa Mulungu
Feb 21, 2024
Mau Auuluridwa /Afotokonzeredwa
Feb 20, 2024
Chilango Cha Amidyani, Rubeni Ndi Gadi Afuna Dziko Lawo, lamulo La Kutenga Dziko, Malire A Dziko Lamalonjezano, Midzi Ya Alevi Ndi Lamulo Lacholowa
Feb 19, 2024
Kupitiliza Kuona Za Lamulo La Kaperekedwe Ka Nsembe, Ndi Malumbiro
Feb 16, 2024
Cholowa Cha Wana Wa Akazi, Mose Akonzekera Kufa, Zopereka Ndi Kulambira Koona
Feb 15, 2024
Ulosi Wachinayi, Nzeru Ya Balamu Ndi Chiwerengero Cha M’badwo Watsopano
Feb 14, 2024
Balaki Afuna Baalamu Kuti Atemberere Israyeli, Koma Baalamu Adalitsa Israyeli
Feb 13, 2024
Chigonjetso Cha A Israyeli, Kudandaula Kwa Chisanu Ndi Chitatu, Njoka Ya Mkuwa, Nyimbo Yachiyamiko Ndi Za Balak Ndi Balaamu
Feb 12, 2024
Kudandaula Pa Kadeshi, Madzi Aturuka
Feb 09, 2024
Aroni Ndi Alevi Akhazikitsidwa Pa Ntchito Yawo, Ndi Kuunika Udindo Wawo
Feb 08, 2024
Kuukira Kwa Kukulu Ndikutsatira Chilango Chachikulu, Komanso Kuukanso Kwa Aroni
Feb 07, 2024
Kuunikanso Kuti Chikonzero Cha Yehova Sichidaonongeke, Chilango Cha Imfa Posasunga Sabata, Kuukira Kwa Kora
Feb 06, 2024
Mose Atuma Akazonde, Israyeli Sakukhulupilira Mulungu, Chilango Cha Mulungu Ndi Kulapa Kwa Israyeli
Feb 05, 2024
Mana, Mose Adandaula, Mulungu
Feb 02, 2024
Malipenga A Siliver, Mpongozi Wa Mose Ndipo A Israyeli Ayamba Kuyenda Ndipo Adandaula
Feb 01, 2024
Kuwala Kuchokera Kuchoyikapo Nyali, Alevi Ayeretsedwa, Paskha Ndi Kutsogoleredwa Kwa Israyeli
Jan 31, 2024
Kufunika Kwa Lumbiro La Unanziri Ndi Madalitso Autatu Wa Mulungu Ndi mphatso zake
Jan 30, 2024
Kudetsedwa Kudzera Mwa Nthenda Ndi Uchimo
Jan 29, 2024
Pfuko La Alevi Pamodzi Ndi Ntchito Yawo, Lipatsidwa Kwa Wansembe Wamkulu
Jan 26, 2024
Mtsitsi Kapena Muzu Wa Ana A Israyeli Ndi Kakhalidwe Kadongosolo Ka Pa Chigono
Jan 25, 2024
Chiyambi Cha Bukhu Ndi Kuwerengedwa Kwa Ana A Israyeli
Jan 24, 2024
Yesu Adziwonetsa Kwa Anthu Ambiri Ndi Kukwera Kumwamba
Jan 23, 2024
Yesu Ayikidwa M’manda Ndi Kuuka Kwa Akufa
Jan 22, 2024
Yesu Achoka Kubwalo La Milandu Kupita Kukapachikidwa
Jan 19, 2024
Amgwira Yesu Ndipo Apita Naye Kumabwalo Ya Mirandu
Jan 18, 2024
Zochitika Zomwe Zikuonetsa Kumalizika Kwa Utumiki Wa Yesu
Jan 17, 2024
Yesu Ayankha Funso Lakuti Kodi Zinthu Izi Zidzaoneka Liti?
Jan 16, 2024
Yesu Akufunsidwa Za Ulamuliro Wake Ndipo Yesu Akuwayankha
Jan 15, 2024
Yesu Alirira Mzinda Wa Yerusalemu
Jan 12, 2024
Yesu Aphunzitsa Kupyolera M’mafanizo Osiyana Siyana Komanso Adalitsa Wana
Jan 11, 2024
Yesu Alangiza Wophunzira Onse
Jan 10, 2024
Fanizo La Kapitawo Wonyenga Ndi Yankho La Yesu Kwa Afarisi
Jan 09, 2024
Yesu Akuphunzitsa Kudzera M’mafanizo A Nkhosa Yosokera, Ndalama Yotayika, Ndi Wana Awiri Wolowerera
Jan 08, 2024
Yesu Aphunzitsa Kudzera M’mafanizo Osiyana-Siyana
Jan 05, 2024
Yesu Akupitiliza Kuphunzitsa Ndi Kuchilitsa Pa Ulendo Waku Yerusalemu
Jan 04, 2024
Yesu Aphunzitsa Ndi Mafanizo Ambiri
Jan 03, 2024
Yesu Aphunzitsa Za Pemphero Komanso Adzudzula Afarisi
Jan 02, 2024
Fanizo La Msamariya Wachifundo
Jan 01, 2024
Ulendo Wa Yesu Ku Yerusalemu
Dec 29, 2023
Yesu Aphunzitsa Kudzera M’mafanizo
Dec 28, 2023
Machilitso, Kuukitsa Akufa Ndi Kuyamikira Yohane M’batizi
Dec 27, 2023
Kusankha Ophunzira Khumi Ndi Awiri Ndi Chiphunzitso Chapachigwa
Dec 26, 2023
Yesu Asankha Ophunzira, Achiritsa Ndi Kuphunzitsa
Dec 25, 2023
Yesu Akanidwa Ndi Abale Wake
Dec 22, 2023
Yohane M’batizi; Kuunika Muzu WaMariya, Komanso Kuyesedwa Kwa Yesu
Dec 21, 2023
Simeoni Ndi Anna Azindikira Mesiya; M’nyamata Yesu Ali M’kachisi; Kuyambika Kwa Utumiki Wa Yohane
Dec 20, 2023
Zinthu Zomwe Zinachitika Kwa Mariya
Dec 19, 2023
Nyimbo Za Khisimisi
Dec 18, 2023
Kulengeza Kwa M’ngelo Gabrieli
Dec 15, 2023
Chiyambi Ndi Kuonetsa Cholinga Cha Bukhuli
Dec 14, 2023
Kugwiritsa Ntchito Pangano
Dec 13, 2023
Tsogolo La Mtundu Wa Israyeli
Dec 12, 2023
Chaka Chopuma Ndi Chaka Chachikondwerero
Dec 11, 2023
Choyikapo Nyali Ndi Mkate Woonekera
Dec 08, 2023
Kupitiliza Kuona Za Nyengo Yopatulika
Dec 07, 2023
Nyengo Kapena Nthawi Yopatulika
Dec 06, 2023
Kudetsedwa Kwa Unsembe Ndi Maliro
Dec 05, 2023
Chilango Cha Kupha
Dec 04, 2023
Ubale Wa Munthu
Dec 01, 2023
Makhalidwe Oyenera Ya Ana Amulungu
Nov 30, 2023
Pali Malo Amodzi Operekera Nsembe
Nov 29, 2023
Tsiku Lotetezera
Nov 28, 2023
Kuunika Zo Ukha
Nov 27, 2023
Mabala Akukha Kapena Mabala Otuluka Magazi
Nov 24, 2023
Mwambo Woyeretsa Munthu Wakhate
Nov 23, 2023
Kupitiliza Kuona Nkhani Ya Khate
Nov 22, 2023
Tikambirana Za Nthenda Ya Khate
Nov 21, 2023
Kutengera Uchimo Kuchokera Kwa Makolo Kapena Kuti Kupatsirana Machimo Kuchokera Kwa Makolo
Nov 20, 2023
Nyama Zodetsedwa Ndi Zosadetsedwa
Nov 17, 2023
Chakudya Cha Anthu A Mulungu
Nov 16, 2023
Mulungu Athana Ndi Kugalukira Ndi Kusamvera
Nov 15, 2023
Ntchito Ya Tsiku Ndi Tsiku Ya Ansembe
Nov 14, 2023
Kupatulika Kwa Ansembe
Nov 13, 2023
Nsembe Yopalamula Ndi Nsembe Ya Mtendere
Nov 10, 2023
Kuunika Za Nsembe Yopalamula
Nov 09, 2023
Zochimwa Za Mtundu Wonse Wa Israyeli, Mtsogoleri Ndi Anthu Wamba
Nov 08, 2023
Nsembe Ya Uchimo Pochimwa Wansembe
Nov 07, 2023
Nsembe Ya Mtendere
Nov 06, 2023
Nsembe Ya Ufa Ndi Ya Zipatso Zoyamba
Nov 03, 2023
Malamulo, Mwambo Ndi Chifukwa Chopereka Yopsereza
Nov 02, 2023
Chiyambi Cha Bukhu La Levitiko Ndi Za Nsembe Yopsereza
Nov 01, 2023
Yesu Auka Kwa Akufa Ndi Kukwera Kumwamba
Oct 31, 2023
Yesu Aperekedwa Nsembe
Oct 30, 2023
Yesu Ali Panjira Yokapachikidwa
Oct 27, 2023
Mgwirizano Wodabwitsa Pakati Pa Kumwamba Ndi Gehena
Oct 26, 2023
Chiphunzitso Cha Paphiri La Oliveti- Zisonyezo Za Kutha Kwa Nyengo
Oct 25, 2023
Yesu Ayesedwa
Oct 24, 2023